Yobu 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Panopa bwenzi nditagona kuti ndisasokonezedwe,+Bwenzi ndili m’tulo pa nthawiyo, ndipo bwenzi pano ndikupuma+ Yobu 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Munthu wobadwa kwa mkazi,+Amakhala ndi moyo waufupi,+ wodzaza ndi masautso.+
13 Panopa bwenzi nditagona kuti ndisasokonezedwe,+Bwenzi ndili m’tulo pa nthawiyo, ndipo bwenzi pano ndikupuma+ Yobu 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Munthu wobadwa kwa mkazi,+Amakhala ndi moyo waufupi,+ wodzaza ndi masautso.+