Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 30:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Pakuti ndikudziwa bwino kuti mudzandibwezera ku imfa,+

      Kunyumba yosonkhanako aliyense wamoyo.

  • Mlaliki 3:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Zonse zimapita kumalo amodzi.+ Zonse zinachokera kufumbi+ ndipo zonse zimabwerera kufumbi.+

  • Ezekieli 18:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Tamverani! Miyoyo yonse ndi yanga.+ Moyo+ wa bambo komanso moyo wa mwana, yonse ndi yanga.+ Moyo umene ukuchimwawo+ ndi umene udzafe.+

  • Aroma 5:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndiye chifukwa chake monga mmene uchimo unalowera m’dziko kudzera mwa munthu mmodzi,+ ndi imfa+ kudzera mwa uchimo, imfayo n’kufalikira kwa anthu onse chifukwa onse anachimwa+ . . .

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena