Mlaliki 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ntchito yonse imene anthu amaigwira mwakhama amagwirira pakamwa pawo,+ koma moyo wawo sukhuta. Aefeso 4:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Wakubayo asabenso,+ koma agwire ntchito molimbikira. Agwire ndi manja ake ntchito yabwino,+ kuti akhale ndi kanthu kena kopatsa munthu wosowa.+ 1 Atesalonika 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiponso muyesetse kukhala mwamtendere,+ kusalowerera mu nkhani za eni,+ ndi kugwira ntchito ndi manja anu+ monga mmene tinakulamulirani.
28 Wakubayo asabenso,+ koma agwire ntchito molimbikira. Agwire ndi manja ake ntchito yabwino,+ kuti akhale ndi kanthu kena kopatsa munthu wosowa.+
11 Ndiponso muyesetse kukhala mwamtendere,+ kusalowerera mu nkhani za eni,+ ndi kugwira ntchito ndi manja anu+ monga mmene tinakulamulirani.