Miyambo 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kasupe wa madzi ako akhale wodalitsidwa,+ ndipo usangalale ndi mkazi wapaunyamata wako.+