Mlaliki 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndinanena mumtima mwanga+ kuti: “Mapeto ngati a munthu wopusa+ adzagweranso ineyo ndithu.”+ Choncho kodi ineyo ndinavutikiranji kukhala wanzeru kwambiri+ pa nthawi imene ija? Ndipo ndinanena mumtima mwanga kuti: “Izinso n’zachabechabe.” Mlaliki 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Usakhale wolungama mopitirira muyezo+ kapena kudzionetsera kuti ndiwe wanzeru kwambiri,+ kuopera kuti ungadzibweretsere chiwonongeko.+ 1 Akorinto 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiponso: “Yehova amadziwa kuti maganizo a anthu anzeru ndi opanda pake.”+
15 Ndinanena mumtima mwanga+ kuti: “Mapeto ngati a munthu wopusa+ adzagweranso ineyo ndithu.”+ Choncho kodi ineyo ndinavutikiranji kukhala wanzeru kwambiri+ pa nthawi imene ija? Ndipo ndinanena mumtima mwanga kuti: “Izinso n’zachabechabe.”
16 Usakhale wolungama mopitirira muyezo+ kapena kudzionetsera kuti ndiwe wanzeru kwambiri,+ kuopera kuti ungadzibweretsere chiwonongeko.+