Numeri 20:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pambuyo pake Yehova anauza Mose ndi Aroni kuti: “Chifukwa simunasonyeze chikhulupiriro mwa ine, polephera kundilemekeza+ pamaso pa ana a Isiraeli, simudzaulowetsa mpingowu m’dziko limene ndidzawapatse.”+ 2 Samueli 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iweyo unachita zinthu zimenezi mobisa,+ koma ine ndidzachita zimenezi pamaso pa Isiraeli+ yense, masanasana.’”+
12 Pambuyo pake Yehova anauza Mose ndi Aroni kuti: “Chifukwa simunasonyeze chikhulupiriro mwa ine, polephera kundilemekeza+ pamaso pa ana a Isiraeli, simudzaulowetsa mpingowu m’dziko limene ndidzawapatse.”+
12 Iweyo unachita zinthu zimenezi mobisa,+ koma ine ndidzachita zimenezi pamaso pa Isiraeli+ yense, masanasana.’”+