Nyimbo ya Solomo 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Wachititsa mtima wanga kugunda, iwe mlongo wanga,+ mkwatibwi wanga.+ Wachititsa mtima wanga kugunda ndi diso lako limodzi lokha,+ ndiponso ndi diso limodzi lokha la mkanda wa m’khosi mwako. 1 Timoteyo 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 ndipo akazi achikulire+ ngati amayi ako. Akazi achitsikana uwadandaulire ngati alongo ako,+ ndipo pochita zimenezi usakhale ndi maganizo alionse oipa.
9 Wachititsa mtima wanga kugunda, iwe mlongo wanga,+ mkwatibwi wanga.+ Wachititsa mtima wanga kugunda ndi diso lako limodzi lokha,+ ndiponso ndi diso limodzi lokha la mkanda wa m’khosi mwako.
2 ndipo akazi achikulire+ ngati amayi ako. Akazi achitsikana uwadandaulire ngati alongo ako,+ ndipo pochita zimenezi usakhale ndi maganizo alionse oipa.