Nyimbo ya Solomo 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Iwe amene mtima wanga umakukonda,+ tandiuza kumene umakadyetsera ziweto,+ kumene umakagonetsa ziweto masana. Kodi ndikhalirenji ngati mkazi amene wafunda nsalu ya namalira pakati pa magulu a ziweto za anzako?” Nyimbo ya Solomo 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Wachikondi wanga ndi wanga, ndipo ine ndine wake.+ Iye akudyetsera ziweto msipu+ umene uli pakati pa maluwa am’tchire.+
7 “Iwe amene mtima wanga umakukonda,+ tandiuza kumene umakadyetsera ziweto,+ kumene umakagonetsa ziweto masana. Kodi ndikhalirenji ngati mkazi amene wafunda nsalu ya namalira pakati pa magulu a ziweto za anzako?”
16 “Wachikondi wanga ndi wanga, ndipo ine ndine wake.+ Iye akudyetsera ziweto msipu+ umene uli pakati pa maluwa am’tchire.+