Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 9:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Yapha nyama yake ndipo yasakaniza vinyo wake. Kuwonjezera apo, yayala patebulo pake.+

  • Nyimbo ya Solomo 5:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 “Ndabwera m’munda mwanga,+ iwe mlongo wanga,+ mkwatibwi wanga.+ Ndathyola mule+ wanga limodzi ndi zonunkhiritsa zanga. Ndadya chisa changa cha uchi limodzi ndi uchi wanga.+ Ndamwa vinyo wanga limodzi ndi mkaka wanga.”

      “Idyani, inu anthu okondana! Imwani ndipo muledzere ndi chikondi chimene mukusonyezana.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena