Salimo 45:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiwedi wokongola kwambiri kuposa ana a anthu.+Mawu otuluka m’kamwa mwako ndi osangalatsadi.+N’chifukwa chake Mulungu adzakupatsa madalitso mpaka kalekale.+ Nyimbo ya Solomo 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Kodi wachikondi wako akuposa bwanji achikondi ena onse,+ iwe mkazi wokongola kwambiri kuposa akazi onse?+ Kodi wachikondi wako akuposa bwanji achikondi ena onse, kuti utilumbiritse lumbiro lotereli?”+
2 Ndiwedi wokongola kwambiri kuposa ana a anthu.+Mawu otuluka m’kamwa mwako ndi osangalatsadi.+N’chifukwa chake Mulungu adzakupatsa madalitso mpaka kalekale.+
9 “Kodi wachikondi wako akuposa bwanji achikondi ena onse,+ iwe mkazi wokongola kwambiri kuposa akazi onse?+ Kodi wachikondi wako akuposa bwanji achikondi ena onse, kuti utilumbiritse lumbiro lotereli?”+