2 Mbiri 32:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Nkhani zina+ zokhudza Hezekiya ndi zochita zake zosonyeza kukoma mtima kosatha,+ zinalembedwa m’masomphenya a mneneri Yesaya mwana wa Amozi,+ m’Buku+ la Mafumu a Yuda ndi Isiraeli.
32 Nkhani zina+ zokhudza Hezekiya ndi zochita zake zosonyeza kukoma mtima kosatha,+ zinalembedwa m’masomphenya a mneneri Yesaya mwana wa Amozi,+ m’Buku+ la Mafumu a Yuda ndi Isiraeli.