Deuteronomo 32:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pakuti pa kukwiya kwanga moto wayaka,+Ndipo udzayaka mpaka kukafika ku Manda,* malo a pansi penipeni.+Udzanyeketsa dziko lapansi ndi zipatso zake,+Ndi kuyatsa maziko a mapiri.+ Salimo 18:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Dziko lapansi linayamba kugwedezekera uku ndi uku ndiponso kutekeseka.+Maziko a mapiri anagwedezeka,+Anagwedezekera uku ndi uku chifukwa Mulungu anakwiya.+ Salimo 18:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo ngalande za pansi pa madzi zinaonekera,+Maziko a dziko lapansi anakhala poonekera.+Zinatero chifukwa cha kudzudzula kwanu, inu Yehova, chifukwa cha mphamvu ya mpweya wa m’mphuno mwanu.+
22 Pakuti pa kukwiya kwanga moto wayaka,+Ndipo udzayaka mpaka kukafika ku Manda,* malo a pansi penipeni.+Udzanyeketsa dziko lapansi ndi zipatso zake,+Ndi kuyatsa maziko a mapiri.+
7 Dziko lapansi linayamba kugwedezekera uku ndi uku ndiponso kutekeseka.+Maziko a mapiri anagwedezeka,+Anagwedezekera uku ndi uku chifukwa Mulungu anakwiya.+
15 Ndipo ngalande za pansi pa madzi zinaonekera,+Maziko a dziko lapansi anakhala poonekera.+Zinatero chifukwa cha kudzudzula kwanu, inu Yehova, chifukwa cha mphamvu ya mpweya wa m’mphuno mwanu.+