Yesaya 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 M’tsiku limenelo, chinthu chimene Yehova adzachiphukitse+ chidzakhala chokongoletsera ndi chaulemerero.+ Zipatso za m’dzikolo zidzakhala zonyaditsa+ ndi zokongola kwa Aisiraeli amene adzapulumuke.+ Yesaya 26:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Anthu anu amene anafa adzakhalanso ndi moyo.+ Anthu anga amene anafa adzadzuka ndi kuimirira.+ Inu anthu okhala m’fumbi, dzukani, fuulani mokondwera!+ Pakuti mame anu+ ali ngati mame a maluwa,+ ndipo dziko lapansi lidzabereka anthu amene anafa.+ Yohane 11:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Marita anati: “Ndikudziwa kuti adzauka pa kuuka kwa akufa+ m’tsiku lomaliza.”
2 M’tsiku limenelo, chinthu chimene Yehova adzachiphukitse+ chidzakhala chokongoletsera ndi chaulemerero.+ Zipatso za m’dzikolo zidzakhala zonyaditsa+ ndi zokongola kwa Aisiraeli amene adzapulumuke.+
19 “Anthu anu amene anafa adzakhalanso ndi moyo.+ Anthu anga amene anafa adzadzuka ndi kuimirira.+ Inu anthu okhala m’fumbi, dzukani, fuulani mokondwera!+ Pakuti mame anu+ ali ngati mame a maluwa,+ ndipo dziko lapansi lidzabereka anthu amene anafa.+