Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Hoseya 13:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “Ine ndidzawawombola ku Manda*+ ndiponso ku imfa.+ Iwe Imfa amene umabweretsa ululu woopsa, kodi mphamvu yako ili kuti?+ Iwe Manda amene umawononga, kodi uli kuti?+ Koma Efuraimu sindimumverabe chisoni.+

  • Yohane 5:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 ndipo adzatuluka. Amene anali kuchita zabwino adzauka kuti alandire moyo.+ Amene anali kuchita zoipa adzauka kuti aweruzidwe.+

  • Machitidwe 24:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ndipo ine ndili ndi chiyembekezo+ mwa Mulungu, chimenenso anthu awa ali nacho, kuti kudzakhala kuuka+ kwa olungama+ ndi osalungama omwe.+

  • 1 Akorinto 15:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Pakuti monga mwa Adamu onse akufa,+ momwemonso mwa Khristu onse adzapatsidwa+ moyo.

  • Chivumbulutso 20:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndiye ndinaona akufa, olemekezeka ndi onyozeka,+ ataimirira pamaso pa mpando wachifumuwo, ndipo mipukutu inafunyululidwa. Koma mpukutu wina unafunyululidwa, ndiwo mpukutu wa moyo.+ Ndipo akufa anaweruzidwa malinga ndi zolembedwa m’mipukutuyo, mogwirizana ndi ntchito zawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena