Ekisodo 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pa nthawiyo Mose ndi ana a Isiraeli anayamba kuimbira Yehova nyimbo iyi, kuti:+“Ndiimbira Yehova, pakuti iye wakwezeka koposa.+Waponyera m’nyanja mahatchi ndi okwera pamahatchiwo.+ 2 Samueli 22:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Davide analankhula ndi Yehova mawu a nyimbo iyi,+ pa tsiku limene Yehova anamulanditsa kwa adani ake+ onse ndiponso m’manja mwa Sauli.+ Salimo 146:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndidzatamanda Yehova pamene ndili moyo.+Ndidzaimbira Mulungu wanga nyimbo zomutamanda kwa moyo wanga wonse.+ Salimo 150:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mutamandeni ndi chinganga cha mawu osangalatsa.+Mutamandeni ndi chinganga cha mawu amphamvu.+ Yesaya 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Muimbireni nyimbo Yehova+ chifukwa wachita zopambana.+ Zimenezi zikulengezedwa m’dziko lonse lapansi.
15 Pa nthawiyo Mose ndi ana a Isiraeli anayamba kuimbira Yehova nyimbo iyi, kuti:+“Ndiimbira Yehova, pakuti iye wakwezeka koposa.+Waponyera m’nyanja mahatchi ndi okwera pamahatchiwo.+
22 Davide analankhula ndi Yehova mawu a nyimbo iyi,+ pa tsiku limene Yehova anamulanditsa kwa adani ake+ onse ndiponso m’manja mwa Sauli.+
2 Ndidzatamanda Yehova pamene ndili moyo.+Ndidzaimbira Mulungu wanga nyimbo zomutamanda kwa moyo wanga wonse.+
5 Muimbireni nyimbo Yehova+ chifukwa wachita zopambana.+ Zimenezi zikulengezedwa m’dziko lonse lapansi.