Yesaya 35:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pa nthawiyo, munthu wolumala adzakwera phiri ngati mmene imachitira mbawala yamphongo.+ Lilime la munthu wosalankhula lidzafuula mokondwa.+ Pakuti m’chipululu mudzatumphuka madzi ndipo m’dera lachipululu mudzayenda mitsinje. Yesaya 41:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndidzatsegula mitsinje pamapiri opanda zomera zilizonse, ndipo pakatikati pa zigwa ndidzatsegulapo akasupe.+ Chipululu ndidzachisandutsa dambo lamadzi, ndipo dziko lopanda madzi ndidzalisandutsa pochokera madzi.+ Yesaya 58:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova azidzakutsogolerani+ nthawi zonse+ ndipo adzakukhutiritsani ngakhale m’dziko louma.+ Iye adzatsitsimula mafupa anu+ ndipo inu mudzakhala ngati munda wachinyontho chokwanira bwino,+ ndiponso ngati kasupe wamadzi yemwe madzi ake sanama.
6 Pa nthawiyo, munthu wolumala adzakwera phiri ngati mmene imachitira mbawala yamphongo.+ Lilime la munthu wosalankhula lidzafuula mokondwa.+ Pakuti m’chipululu mudzatumphuka madzi ndipo m’dera lachipululu mudzayenda mitsinje.
18 Ndidzatsegula mitsinje pamapiri opanda zomera zilizonse, ndipo pakatikati pa zigwa ndidzatsegulapo akasupe.+ Chipululu ndidzachisandutsa dambo lamadzi, ndipo dziko lopanda madzi ndidzalisandutsa pochokera madzi.+
11 Yehova azidzakutsogolerani+ nthawi zonse+ ndipo adzakukhutiritsani ngakhale m’dziko louma.+ Iye adzatsitsimula mafupa anu+ ndipo inu mudzakhala ngati munda wachinyontho chokwanira bwino,+ ndiponso ngati kasupe wamadzi yemwe madzi ake sanama.