Salimo 94:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kodi amene amalangiza mitundu ya anthu,+Amene amaphunzitsa anthu kuti akhale ozindikira, sangathe kudzudzula?+ Miyambo 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti ndithu ndidzakupatsani malangizo abwino.+ Musasiye lamulo langa.+
10 Kodi amene amalangiza mitundu ya anthu,+Amene amaphunzitsa anthu kuti akhale ozindikira, sangathe kudzudzula?+