Salimo 76:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu ndinu wochititsa mantha,+Ndani angaime pamaso panu inu mutakwiya kwambiri?+ Yesaya 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Lowani muthanthwe ndipo dzibiseni m’fumbi chifukwa cha kuopsa kwa Yehova, ndiponso chifukwa cha ulemerero ndi ukulu wake.+ Luka 23:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 M’masiku amenewo iwo adzayamba kuuza mapiri kuti, ‘Tigwereni!’ ndipo adzauza zitunda kuti, ‘Tikwirireni!’+ 2 Atesalonika 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Amenewa adzawaweruza kuti alandire chilango+ cha chiwonongeko chamuyaya,+ kuwachotsa pamaso pa Ambuye ndi ku ulemerero wa mphamvu zake.+ Chivumbulutso 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mafumu a dziko lapansi, nduna, akuluakulu a asilikali, olemera, amphamvu, kapolo aliyense ndi mfulu aliyense, anabisala m’mapanga ndi m’matanthwe+ a m’mapiri.
10 Lowani muthanthwe ndipo dzibiseni m’fumbi chifukwa cha kuopsa kwa Yehova, ndiponso chifukwa cha ulemerero ndi ukulu wake.+
30 M’masiku amenewo iwo adzayamba kuuza mapiri kuti, ‘Tigwereni!’ ndipo adzauza zitunda kuti, ‘Tikwirireni!’+
9 Amenewa adzawaweruza kuti alandire chilango+ cha chiwonongeko chamuyaya,+ kuwachotsa pamaso pa Ambuye ndi ku ulemerero wa mphamvu zake.+
15 Mafumu a dziko lapansi, nduna, akuluakulu a asilikali, olemera, amphamvu, kapolo aliyense ndi mfulu aliyense, anabisala m’mapanga ndi m’matanthwe+ a m’mapiri.