Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 94:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Pakuti zigamulo zidzayambiranso kukhala zachilungamo,+

      Ndipo onse owongoka mtima adzazitsatira.

  • Yesaya 42:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Iye sadzatsala pang’ono kuzima kapena kuphwanyidwa mpaka atakhazikitsa chilungamo padziko lapansi.+ Zilumba zidzadikirira lamulo lake.+

  • Yesaya 60:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Anthu ako onse adzakhala olungama.+ Iwo adzakhala m’dzikomo mpaka kalekale.+ Anthuwo adzakhala mmera wobzalidwa ndi ine+ ndiponso ntchito ya manja anga,+ kuti ineyo ndikongoletsedwe.+

  • Tito 2:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Zimenezi zatiphunzitsa kukana moyo wosaopa Mulungu+ ndi zilakolako za dziko,+ koma kukhala amaganizo abwino, achilungamo ndi odzipereka kwa Mulungu+ m’nthawi* ino.+

  • 2 Petulo 3:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Koma pali kumwamba kwatsopano+ ndi dziko lapansi latsopano+ zimene ife tikuyembekezera mogwirizana ndi lonjezo lake, ndipo mmenemo mudzakhala chilungamo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena