Yesaya 26:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Pakuti iye watsitsa anthu okhala pamalo okwezeka,+ okhala m’mudzi wokwezeka.+ Mudziwo wautsitsa. Wautsitsira pansi, waugwetsa mpaka pafumbi.+
5 “Pakuti iye watsitsa anthu okhala pamalo okwezeka,+ okhala m’mudzi wokwezeka.+ Mudziwo wautsitsa. Wautsitsira pansi, waugwetsa mpaka pafumbi.+