Yesaya 35:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pa nthawi imeneyo, maso a anthu akhungu adzatsegulidwa,+ ndipo makutu a anthu ogontha adzayamba kumva.+ Mateyu 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Khamu lalikulu la anthu linam’tsatira, ndipo iye anawachiritsa kumeneko.+ Maliko 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Popeza kuti anali atachiritsa anthu ambiri, onse amene anali ndi matenda aakulu anali kudziponya kwa iye kuti angomukhudza.+ Maliko 7:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kumeneko anthu anam’bweretsera munthu wogontha komanso wovutika kulankhula. Iwo anamupempha kuti aike dzanja lake pa munthuyo.+
5 Pa nthawi imeneyo, maso a anthu akhungu adzatsegulidwa,+ ndipo makutu a anthu ogontha adzayamba kumva.+
10 Popeza kuti anali atachiritsa anthu ambiri, onse amene anali ndi matenda aakulu anali kudziponya kwa iye kuti angomukhudza.+
32 Kumeneko anthu anam’bweretsera munthu wogontha komanso wovutika kulankhula. Iwo anamupempha kuti aike dzanja lake pa munthuyo.+