Ezara 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pa nthawi yopereka nsembe yambewu+ yamadzulo, pambuyo podzichepetsa mwanjira imeneyi, ndinaimirira, zovala zanga zitang’ambika, ndipo ndinagwada+ n’kutambasulira manja anga kwa Yehova Mulungu wanga.+ Salimo 123:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 123 Ndakweza maso anga kuyang’ana inu,+Kuyang’ana inu amene mukukhala kumwamba.+ Danieli 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndinayang’ana+ kwa Yehova Mulungu woona kuti ndimufunefune mwa kupemphera,+ kumuchonderera, kusala kudya, kuvala ziguduli* ndi kudzithira phulusa.+
5 Pa nthawi yopereka nsembe yambewu+ yamadzulo, pambuyo podzichepetsa mwanjira imeneyi, ndinaimirira, zovala zanga zitang’ambika, ndipo ndinagwada+ n’kutambasulira manja anga kwa Yehova Mulungu wanga.+
3 Ndinayang’ana+ kwa Yehova Mulungu woona kuti ndimufunefune mwa kupemphera,+ kumuchonderera, kusala kudya, kuvala ziguduli* ndi kudzithira phulusa.+