Yobu 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inenso ndikanatha kulankhula ngati mmene mukuchitiramu,Moyo wanu ukanakhala ngati mmene ulili moyo wanga,Kodi ndikanalankhula mawu ogometsa okunenani?+Ndipo kodi ndikanakupukusirani mutu?+ Salimo 22:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu onse ondiona amandinyodola.+Iwo amandinyogodola ndi pakamwa pawo, ndipo amapukusa mitu yawo mondinyoza.+ Iwo amati: Salimo 109:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kwa iwo ndakhala chinthu choyenera kutonzedwa.+Akandiona amapukusa mitu yawo.+
4 Inenso ndikanatha kulankhula ngati mmene mukuchitiramu,Moyo wanu ukanakhala ngati mmene ulili moyo wanga,Kodi ndikanalankhula mawu ogometsa okunenani?+Ndipo kodi ndikanakupukusirani mutu?+
7 Anthu onse ondiona amandinyodola.+Iwo amandinyogodola ndi pakamwa pawo, ndipo amapukusa mitu yawo mondinyoza.+ Iwo amati: