Genesis 30:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Rakele anakhala ndi pakati n’kubereka mwana wamwamuna. Ndiyeno iye anati: “Mulungu wandichotsera chitonzo.”+ Yesaya 54:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Usachite mantha,+ pakuti sudzachititsidwa manyazi.+ Usachite manyazi, pakuti sudzakhumudwitsidwa.+ Iwe udzaiwala ngakhale manyazi a paubwana wako,+ ndipo sudzakumbukiranso kunyozeka kwa paumasiye wako wa nthawi yaitali.” Luka 1:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Izitu n’zimene Yehova wandichitira masiku ano pamene wandicheukira kuti andichotsere chitonzo pamaso pa anthu.”+
23 Rakele anakhala ndi pakati n’kubereka mwana wamwamuna. Ndiyeno iye anati: “Mulungu wandichotsera chitonzo.”+
4 Usachite mantha,+ pakuti sudzachititsidwa manyazi.+ Usachite manyazi, pakuti sudzakhumudwitsidwa.+ Iwe udzaiwala ngakhale manyazi a paubwana wako,+ ndipo sudzakumbukiranso kunyozeka kwa paumasiye wako wa nthawi yaitali.”
25 “Izitu n’zimene Yehova wandichitira masiku ano pamene wandicheukira kuti andichotsere chitonzo pamaso pa anthu.”+