Yeremiya 31:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Nditabwerera kwa inu ndinadzimvera chisoni.+ Mutandithandiza kuzindikira ndinadzimenya pantchafu chifukwa cha chisoni.+ Ndinachita manyazi ndipo ndinanyazitsidwa+ chifukwa cha chitonzo cha paubwana wanga.’”+ Ezekieli 16:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 M’zonyansa zako zonse ndi m’zochita zako zauhule sunakumbukire masiku a ubwana wako pamene unali wosavala ndi wamaliseche, pamene unali kuponyaponya timiyendo tako m’mwamba uli m’magazi ako.+ Ezekieli 16:60 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 60 Ndithu ine ndidzakumbukira pangano limene ndinapangana ndi iwe m’masiku a ubwana wako,+ ndipo ndidzakukhazikitsira pangano limene lidzakhalepo mpaka kalekale.*+
19 Nditabwerera kwa inu ndinadzimvera chisoni.+ Mutandithandiza kuzindikira ndinadzimenya pantchafu chifukwa cha chisoni.+ Ndinachita manyazi ndipo ndinanyazitsidwa+ chifukwa cha chitonzo cha paubwana wanga.’”+
22 M’zonyansa zako zonse ndi m’zochita zako zauhule sunakumbukire masiku a ubwana wako pamene unali wosavala ndi wamaliseche, pamene unali kuponyaponya timiyendo tako m’mwamba uli m’magazi ako.+
60 Ndithu ine ndidzakumbukira pangano limene ndinapangana ndi iwe m’masiku a ubwana wako,+ ndipo ndidzakukhazikitsira pangano limene lidzakhalepo mpaka kalekale.*+