Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 20:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “Usadzipangire fano kapena chifaniziro cha chinthu chilichonse chakumwamba, kapena chapadziko lapansi, kapenanso cham’madzi a padziko lapansi.*+

  • Deuteronomo 4:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “Chotero musamale moyo wanu,+ chifukwa pa tsiku limene Yehova analankhula nanu kuchokera pakati pa moto ku Horebe, simunaone kalikonse+ m’motomo.

  • Deuteronomo 4:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Musamale kuti musachite zinthu zokuwonongetsani,+ kutinso musadzipangire chifaniziro, chifaniziro cha chinthu chilichonse, chachimuna kapena chachikazi,+

  • Machitidwe 17:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 “Popeza kuti ndife mbadwa za Mulungu,+ tisaganize kuti Mulunguyo+ ali ngati golide, siliva, mwala kapena chilichonse chosemedwa mwa luso ndi nzeru za munthu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena