Salimo 139:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kwa ine ndi zovuta kwambiri kuti ndidziwe zinthu zonsezi.+Ndi zapamwamba kwambiri moti sindingathe kuzifikira.+ Salimo 147:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ambuye wathu ndi wamkulu ndipo ali ndi mphamvu zochuluka.+Nzeru zake zilibe malire.+ Yesaya 55:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Pakuti monga momwe kumwamba kulili pamwamba kuposa dziko lapansi,+ momwemonso njira zanga n’zapamwamba kuposa njira zanu,+ ndiponso maganizo anga ndi apamwamba kuposa maganizo anu.+ Aroma 11:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ndithudi, madalitso amene Mulungu amapereka ndi ochuluka kwambiri.+ Nzeru+ zake n’zozama, ndiponso iye ndi wodziwa zinthu kwambiri.+ Ziweruzo zake ndi zosasanthulika,+ ndipo ndani angatulukire njira zake? 1 Akorinto 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakuti “ndani akudziwa maganizo a Yehova+ kuti amulangize?”+ Koma ifeyo tili ndi maganizo+ a Khristu.
6 Kwa ine ndi zovuta kwambiri kuti ndidziwe zinthu zonsezi.+Ndi zapamwamba kwambiri moti sindingathe kuzifikira.+
9 “Pakuti monga momwe kumwamba kulili pamwamba kuposa dziko lapansi,+ momwemonso njira zanga n’zapamwamba kuposa njira zanu,+ ndiponso maganizo anga ndi apamwamba kuposa maganizo anu.+
33 Ndithudi, madalitso amene Mulungu amapereka ndi ochuluka kwambiri.+ Nzeru+ zake n’zozama, ndiponso iye ndi wodziwa zinthu kwambiri.+ Ziweruzo zake ndi zosasanthulika,+ ndipo ndani angatulukire njira zake?
16 Pakuti “ndani akudziwa maganizo a Yehova+ kuti amulangize?”+ Koma ifeyo tili ndi maganizo+ a Khristu.