Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 25:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Pakuti inu mwakhala malo achitetezo kwa munthu wonyozeka ndiponso malo achitetezo kwa munthu wosauka m’masautso ake.+ Mwakhala malo ousapo mvula yamkuntho ndi mthunzi+ wobisalirapo kutentha kwa dzuwa. Mwakhala wotero pamene anthu ankhanza akuwomba anzawo ngati mvula yamkuntho yowomba khoma.

  • Yesaya 32:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Aliyense adzakhala ngati malo obisalirapo mphepo ndi malo ousapo mvula yamkuntho,+ ngati mitsinje yamadzi m’dziko lopanda madzi,+ ndiponso ngati mthunzi wa thanthwe lalikulu m’dziko louma.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena