Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 95:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Kwa zaka 40, m’badwo umenewo unali kundinyansa,+

      Ndipo ndinati:

      “Anthu awa mitima yawo imasochera,+

      Ndipo sadziwa njira zanga.”+

  • Yesaya 1:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Moyo wanga ukudana ndi masiku anu okhala mwezi ndi zikondwerero zanu.+ Zimenezi zasanduka katundu wolemera kwa ine,+ ndipo ndatopa kuzinyamula.+

  • Malaki 2:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 “Pali chinthu china chimene anthu inu mukuchita ndipo chikuchititsa kuti guwa lansembe la Yehova lidzaze ndi misozi, kulira ndi kubuula. Chifukwa cha zimenezi, nsembe zanu zimene mumapereka ngati mphatso n’zosavomerezeka kwa iye ndipo sakusangalala ndi chilichonse chochokera m’manja mwanu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena