Yesaya 43:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Iwe sunandigulire bango lonunkhira+ ndi ndalama iliyonse, ndipo sunandikhutitse ndi mafuta a nsembe zako.+ Koma m’malomwake, wandiumiriza ndi machimo ako kuti ndikutumikire. Wanditopetsa ndi zolakwa zako.+
24 Iwe sunandigulire bango lonunkhira+ ndi ndalama iliyonse, ndipo sunandikhutitse ndi mafuta a nsembe zako.+ Koma m’malomwake, wandiumiriza ndi machimo ako kuti ndikutumikire. Wanditopetsa ndi zolakwa zako.+