Genesis 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kwa Adamu, Mulungu ananena kuti: “Chifukwa wamvera mawu a mkazi wako, ndipo wadya chipatso cha mtengo umene ndinakulamula+ kuti, ‘Usadzadye zipatso zake,’ nthaka ikhale yotembereredwa kwa iwe.+ Udzadya zotuluka m’nthakayo movutikira masiku onse a moyo wako.+ Salimo 78:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo asadzakhale ngati makolo awo,+M’badwo wosamva ndi wopanduka,+M’badwo umene sunakonze mtima wawo,+Ndipo maganizo awo sanali okhulupirika kwa Mulungu.+ Aroma 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiye chifukwa chake monga mmene uchimo unalowera m’dziko kudzera mwa munthu mmodzi,+ ndi imfa+ kudzera mwa uchimo, imfayo n’kufalikira kwa anthu onse chifukwa onse anachimwa+ . . .
17 Kwa Adamu, Mulungu ananena kuti: “Chifukwa wamvera mawu a mkazi wako, ndipo wadya chipatso cha mtengo umene ndinakulamula+ kuti, ‘Usadzadye zipatso zake,’ nthaka ikhale yotembereredwa kwa iwe.+ Udzadya zotuluka m’nthakayo movutikira masiku onse a moyo wako.+
8 Ndipo asadzakhale ngati makolo awo,+M’badwo wosamva ndi wopanduka,+M’badwo umene sunakonze mtima wawo,+Ndipo maganizo awo sanali okhulupirika kwa Mulungu.+
12 Ndiye chifukwa chake monga mmene uchimo unalowera m’dziko kudzera mwa munthu mmodzi,+ ndi imfa+ kudzera mwa uchimo, imfayo n’kufalikira kwa anthu onse chifukwa onse anachimwa+ . . .