-
Malaki 1:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 “‘Mwana amalemekeza bambo ake+ ndipo wantchito amalemekeza mbuye wake.+ Ngati ine ndili atate,+ ulemu wanga uli kuti?+ Ngati ndili Ambuye Wamkulu, n’chifukwa chiyani simundiopa?’+ watero Yehova wa makamu kwa inu ansembe amene mukunyoza dzina langa.+
“‘Inu mukunena kuti: “Kodi dzina lanu talinyoza motani?”’
-