1 Timoteyo 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Onse amene ali m’goli laukapolo, aziona kuti ambuye awo ndi oyenera kuwapatsa ulemu wawo wonse,+ kuti dzina la Mulungu ndi chiphunzitsocho asazinenere zoipa.+ Tito 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Akapolo+ azigonjera ambuye awo pa zonse+ ndipo aziwakondweretsa. Asamatsutsane nawo+
6 Onse amene ali m’goli laukapolo, aziona kuti ambuye awo ndi oyenera kuwapatsa ulemu wawo wonse,+ kuti dzina la Mulungu ndi chiphunzitsocho asazinenere zoipa.+