Ekisodo 15:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Zitatero Mose anafuulira Yehova+ ndipo Yehova anam’sonyeza kamtengo. Mose anaponya kamtengoko m’madzi moti madziwo anakhala okoma.+ Pamenepo Mulungu anawakhazikitsira lamulo ndi maziko operekera chiweruzo, ndipo pa nthawiyo anawayesa.+ Ekisodo 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tamvera! Ine ndidzatsogola kukaima pathanthwe ku Horebe.* Kumeneko ukamenye thanthwelo, ndipo padzatuluka madzi amene anthu adzamwa.”+ Chotero Mose anachitadi zomwezo, pamaso pa akulu a Isiraeli, Deuteronomo 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mungaiwale amene anakuyendetsani m’chipululu chachikulu ndi chochititsa mantha,+ chokhala ndi njoka zapoizoni,+ zinkhanira ndiponso dziko louma lopanda madzi. Amenenso anakutulutsirani madzi pamwala wolimba ngati nsangalabwi.+
25 Zitatero Mose anafuulira Yehova+ ndipo Yehova anam’sonyeza kamtengo. Mose anaponya kamtengoko m’madzi moti madziwo anakhala okoma.+ Pamenepo Mulungu anawakhazikitsira lamulo ndi maziko operekera chiweruzo, ndipo pa nthawiyo anawayesa.+
6 Tamvera! Ine ndidzatsogola kukaima pathanthwe ku Horebe.* Kumeneko ukamenye thanthwelo, ndipo padzatuluka madzi amene anthu adzamwa.”+ Chotero Mose anachitadi zomwezo, pamaso pa akulu a Isiraeli,
15 Mungaiwale amene anakuyendetsani m’chipululu chachikulu ndi chochititsa mantha,+ chokhala ndi njoka zapoizoni,+ zinkhanira ndiponso dziko louma lopanda madzi. Amenenso anakutulutsirani madzi pamwala wolimba ngati nsangalabwi.+