Yesaya 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Taonani! Mulungu ndiye chipulumutso changa.+ Ndidzamukhulupirira ndipo sindidzaopa chilichonse,+ pakuti Ya* Yehova ndiye mphamvu zanga+ ndi nyonga zanga,+ ndipo iye wakhala chipulumutso changa.”+ Yesaya 56:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Yehova wanena kuti: “Anthu inu, tsatirani chilungamo+ ndipo chitani zolungama.+ Pakuti chipulumutso changa chatsala pang’ono kubwera,+ ndipo chilungamo changa chatsala pang’ono kuonekera.+
2 Taonani! Mulungu ndiye chipulumutso changa.+ Ndidzamukhulupirira ndipo sindidzaopa chilichonse,+ pakuti Ya* Yehova ndiye mphamvu zanga+ ndi nyonga zanga,+ ndipo iye wakhala chipulumutso changa.”+
56 Yehova wanena kuti: “Anthu inu, tsatirani chilungamo+ ndipo chitani zolungama.+ Pakuti chipulumutso changa chatsala pang’ono kubwera,+ ndipo chilungamo changa chatsala pang’ono kuonekera.+