Salimo 102:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Zimenezi zidzatha, koma inu mudzakhalapobe.+Ndipo zonsezi zidzatha ngati chovala.+Mofanana ndi zovala zimene zatha, mudzapezerapo zina ndipo nazonso zidzatha.+ Yesaya 34:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Makamu onse akumwamba adzawola.+ Kumwamba kudzapindidwa ngati mpukutu wolembapo.+ Makamu onse akumwambawo adzafota ngati mmene masamba amafotera pamtengo wa mpesa n’kuthothoka, ndiponso ngati mmene nkhuyu yonyala imathothokera mumtengo wa mkuyu.+ Aheberi 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zimenezi zidzatha, koma inu mudzakhalapo mpaka muyaya. Ndipo zonsezi zidzatha ngati mmene malaya akunja amathera.+
26 Zimenezi zidzatha, koma inu mudzakhalapobe.+Ndipo zonsezi zidzatha ngati chovala.+Mofanana ndi zovala zimene zatha, mudzapezerapo zina ndipo nazonso zidzatha.+
4 Makamu onse akumwamba adzawola.+ Kumwamba kudzapindidwa ngati mpukutu wolembapo.+ Makamu onse akumwambawo adzafota ngati mmene masamba amafotera pamtengo wa mpesa n’kuthothoka, ndiponso ngati mmene nkhuyu yonyala imathothokera mumtengo wa mkuyu.+
11 Zimenezi zidzatha, koma inu mudzakhalapo mpaka muyaya. Ndipo zonsezi zidzatha ngati mmene malaya akunja amathera.+