Yobu 13:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ine* ndili ngati chinthu chowola chimene chimatha.+Ngati chovala chimene njenjete* zimadya.+ Yesaya 50:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, adzandithandiza. Ndani amene anganene kuti ndine wolakwa?+ Onsewo adzatha ngati chovala.+ Njenjete* idzawadya.+
9 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, adzandithandiza. Ndani amene anganene kuti ndine wolakwa?+ Onsewo adzatha ngati chovala.+ Njenjete* idzawadya.+