Salimo 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano inu mafumu, sonyezani kuzindikira,Lolani kuti maganizo anu akonzedwe, inu oweruza a dziko lapansi.+ Salimo 72:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mafumu onse adzamugwadira ndi kumuweramira.+Ndipo mitundu yonse ya anthu idzamutumikira.+
10 Tsopano inu mafumu, sonyezani kuzindikira,Lolani kuti maganizo anu akonzedwe, inu oweruza a dziko lapansi.+