Salimo 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye wokhala kumwamba+ adzaseka,Yehova adzawanyodola.+ Yesaya 41:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu amene akulimbana nawe udzawafunafuna koma sudzawapeza. Anthu amene akumenyana nawe+ adzakhala ngati kulibeko ndipo sadzakhalanso ngati kanthu.+
12 Anthu amene akulimbana nawe udzawafunafuna koma sudzawapeza. Anthu amene akumenyana nawe+ adzakhala ngati kulibeko ndipo sadzakhalanso ngati kanthu.+