Salimo 119:111 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 111 Ndatenga zikumbutso zanu kukhala chuma changa mpaka kalekale,+Pakuti zimakondweretsa mtima wanga.+ Mlaliki 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Poti zonse zanenedwa, mfundo yaikulu ndi yakuti: Opa Mulungu woona+ ndi kusunga malamulo ake+ chifukwa zimenezi ndiye zimene munthu ayenera kuchita. Machitidwe 10:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Iye amalandira munthu wochokera mu mtundu uliwonse, amene amamuopa ndi kuchita chilungamo.+
111 Ndatenga zikumbutso zanu kukhala chuma changa mpaka kalekale,+Pakuti zimakondweretsa mtima wanga.+
13 Poti zonse zanenedwa, mfundo yaikulu ndi yakuti: Opa Mulungu woona+ ndi kusunga malamulo ake+ chifukwa zimenezi ndiye zimene munthu ayenera kuchita.