Yesaya 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mukatambasula manja anu,+ ndimakubisirani maso anga.+ Ngakhale mupereke mapemphero ambiri,+ ine sindimvetsera.+ Manja anu adzaza magazi amene mwakhetsa.+ Yeremiya 42:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 kwa mneneri Yeremiya ndi kumuuza kuti: “Chonde, tikomere mtima ndipo utipempherere kwa Yehova Mulungu wako.+ Pempherera anthu onse amene atsalawa chifukwa amene tatsala tilipo ochepa monga mmene ukutioneramu, ngakhale kuti tinalipo anthu ambiri.+ Yeremiya 42:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 kuti mwachimwira miyoyo yanu.+ Zili choncho chifukwa inu mwandituma kwa Yehova Mulungu wanu kuti, ‘Tipempherere kwa Yehova Mulungu wathu ndipo udzatiuze zilizonse zimene Yehova Mulungu wathu adzanena ndipo ife tidzachita zomwezo.’+
15 Mukatambasula manja anu,+ ndimakubisirani maso anga.+ Ngakhale mupereke mapemphero ambiri,+ ine sindimvetsera.+ Manja anu adzaza magazi amene mwakhetsa.+
2 kwa mneneri Yeremiya ndi kumuuza kuti: “Chonde, tikomere mtima ndipo utipempherere kwa Yehova Mulungu wako.+ Pempherera anthu onse amene atsalawa chifukwa amene tatsala tilipo ochepa monga mmene ukutioneramu, ngakhale kuti tinalipo anthu ambiri.+
20 kuti mwachimwira miyoyo yanu.+ Zili choncho chifukwa inu mwandituma kwa Yehova Mulungu wanu kuti, ‘Tipempherere kwa Yehova Mulungu wathu ndipo udzatiuze zilizonse zimene Yehova Mulungu wathu adzanena ndipo ife tidzachita zomwezo.’+