Salimo 22:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ofatsa adzadya ndi kukhuta.+Ofunafuna Yehova adzamutamanda.+Mitima yanu ikhale ndi moyo kosatha.+ Salimo 34:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndidzadzitamandira mwa Yehova.+Ofatsa adzamva ndi kukondwera.+ Mateyu 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Akhungu akuonanso,+ olumala+ akuyendayenda, akhate+ akuyeretsedwa ndipo ogontha+ akumva. Akufa+ akuukitsidwa, ndipo kwa aumphawi uthenga wabwino ukulengezedwa.+
5 Akhungu akuonanso,+ olumala+ akuyendayenda, akhate+ akuyeretsedwa ndipo ogontha+ akumva. Akufa+ akuukitsidwa, ndipo kwa aumphawi uthenga wabwino ukulengezedwa.+