Ezekieli 36:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Pa tsiku limene ndidzakuyeretseni kuchotsa zolakwa zanu zonse, ndidzachititsanso kuti m’mizinda yanu mukhale anthu+ ndipo malo owonongeka adzamangidwanso.+
33 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Pa tsiku limene ndidzakuyeretseni kuchotsa zolakwa zanu zonse, ndidzachititsanso kuti m’mizinda yanu mukhale anthu+ ndipo malo owonongeka adzamangidwanso.+