Salimo 115:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Inu ndinu amene mwadalitsidwa ndi Yehova,+Wopanga kumwamba ndi dziko lapansi.+ Yesaya 65:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Sadzagwira ntchito pachabe+ komanso sadzaberekera tsoka,+ chifukwa iwo ndiponso ana awo+ ndi odalitsidwa ndi Yehova.+
23 Sadzagwira ntchito pachabe+ komanso sadzaberekera tsoka,+ chifukwa iwo ndiponso ana awo+ ndi odalitsidwa ndi Yehova.+