9 Ana awo adzadziwika pakati pa mitundu ya anthu,+ ndipo mbadwa zawo zidzadziwika pakati pa anthu osiyanasiyana. Onse owaona adzazindikira+ kuti iwo ndi ana odalitsidwa ndi Yehova.”+
9 Ndidzawamwaza ngati mbewu pakati pa anthu a mitundu ina+ ndipo adzandikumbukira ali kumadera akutali.+ Iwowo ndi ana awo adzapezanso mphamvu ndipo adzabwerera.+