Ekisodo 23:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 M’dziko lanu simudzapezeka mkazi wopititsa padera kapena wosabereka.+ Ndipo ndidzachulukitsa masiku anu.+ Yesaya 33:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Palibe munthu wokhala m’dzikolo amene adzanene kuti: “Ndikudwala.”+ Anthu okhala mmenemo adzakhala amene machimo awo anakhululukidwa.+ Yesaya 54:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ana ako onse+ adzakhala anthu ophunzitsidwa ndi Yehova,+ ndipo mtendere wa ana ako udzakhala wochuluka.+
26 M’dziko lanu simudzapezeka mkazi wopititsa padera kapena wosabereka.+ Ndipo ndidzachulukitsa masiku anu.+
24 Palibe munthu wokhala m’dzikolo amene adzanene kuti: “Ndikudwala.”+ Anthu okhala mmenemo adzakhala amene machimo awo anakhululukidwa.+
13 Ana ako onse+ adzakhala anthu ophunzitsidwa ndi Yehova,+ ndipo mtendere wa ana ako udzakhala wochuluka.+