1 Mafumu 8:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “Koma kodi Mulungu angakhaledi padziko lapansi?+ Taonani! Kumwamba,+ ngakhale kumwambamwamba,+ simungakwaneko.+ Kuli bwanji nyumba+ imene ndamangayi? Yesaya 66:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 66 Yehova wanena kuti: “Kumwamba ndiko mpando wanga wachifumu,+ ndipo dziko lapansi ndilo chopondapo mapazi anga.+ Kodi anthu inu mungandimangire nyumba yotani?+ Ndipo malo oti ine ndingapumulirepo, ali kuti?”+ Machitidwe 7:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Ngakhale ndi choncho, Wam’mwambamwamba sakhala m’nyumba zomangidwa ndi manja,+ monga mneneri akunenera kuti,
27 “Koma kodi Mulungu angakhaledi padziko lapansi?+ Taonani! Kumwamba,+ ngakhale kumwambamwamba,+ simungakwaneko.+ Kuli bwanji nyumba+ imene ndamangayi?
66 Yehova wanena kuti: “Kumwamba ndiko mpando wanga wachifumu,+ ndipo dziko lapansi ndilo chopondapo mapazi anga.+ Kodi anthu inu mungandimangire nyumba yotani?+ Ndipo malo oti ine ndingapumulirepo, ali kuti?”+
48 Ngakhale ndi choncho, Wam’mwambamwamba sakhala m’nyumba zomangidwa ndi manja,+ monga mneneri akunenera kuti,