Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 4:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 anthu okhala mu mdima+ anaona kuwala kwakukulu,+ ndipo anthu okhala m’dera la mthunzi wa imfa, kuwala+ kunawatulukira.”+

  • Luka 1:79
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 79 ndipo kudzaunikira amene akhala mu mdima ndi mu mthunzi wa imfa,+ ndi kutsogolera bwinobwino mapazi athu panjira yamtendere.”

  • Luka 2:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Maso anga aona kuwala+ kochotsa nsalu yophimba+ mitundu ya anthu+ ndi ulemerero wa anthu anu Aisiraeli.”

  • Yohane 1:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Kuwala+ kwenikweni kumene kumaunikira+ anthu osiyanasiyana+ kunali pafupi kubwera m’dziko.

  • Yohane 8:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pamenepo Yesu analankhula nawonso kuti: “Ine ndine kuwala+ kwa dziko. Wonditsatira ine sadzayenda mumdima,+ koma adzakhala nako kuwala kwa moyo.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena