Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 32:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Kubwezera ndi kwanga, chilangonso ndi changa.+

      Pa nthawi yoikidwiratu phazi lawo lidzaterereka poyenda,+

      Pakuti tsiku la tsoka lawo layandikira,+

      Ndipo zowagwera zikufika mofulumira.’+

  • Mlaliki 3:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Chilichonse chili ndi nthawi yake,+ ndipo chilichonse chochitika padziko lapansi chilidi ndi nthawi yake:

  • Yeremiya 51:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Mwana wamkazi wa Babulo ali ngati malo opunthira mbewu.+ Ino ndi nthawi yomupondaponda. Koma kwatsala ka nthawi pang’ono kuti nthawi yokolola imufikire.”+

  • 2 Petulo 2:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Komanso chifukwa chosirira mwansanje, adzakudyerani masuku pamutu ndi mawu achinyengo.+ Koma chiweruzo chawo chimene chinagamulidwa kalekale+ chikubwera mofulumira, ndipo chiwonongeko chawo sichikuzengereza.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena