Ekisodo 9:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pa nthawi imeneyo mbewu za fulakesi* ndi balere zinawonongeka, chifukwa balere anali atacha ndipo fulakesi anali atachita maluwa.+ Miyambo 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndayala zofunda pabedi panga. Ndayalaponso nsalu za ku Iguputo zamitundu yosiyanasiyana.+
31 Pa nthawi imeneyo mbewu za fulakesi* ndi balere zinawonongeka, chifukwa balere anali atacha ndipo fulakesi anali atachita maluwa.+